Nehemiya 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mʼmasiku amenewo, anthu olemekezeka+ a mu Yuda ankalemba makalata ambiri opita kwa Tobia ndipo Tobiayo ankawayankha.
17 Mʼmasiku amenewo, anthu olemekezeka+ a mu Yuda ankalemba makalata ambiri opita kwa Tobia ndipo Tobiayo ankawayankha.