Nehemiya 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komanso anthu amenewa nthawi zonse ankandiuza zinthu zabwino za Tobia. Kenako ankatenga zimene ine ndanena nʼkukamuuza Tobiayo ndipo iye ankanditumizira makalata ondiopseza.+
19 Komanso anthu amenewa nthawi zonse ankandiuza zinthu zabwino za Tobia. Kenako ankatenga zimene ine ndanena nʼkukamuuza Tobiayo ndipo iye ankanditumizira makalata ondiopseza.+