Nehemiya 7:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Amenewa ndi amene mayina awo anawayangʼana mʼkaundula kuti atsimikizire za mzere wawo wobadwira koma sanapezekemo. Choncho anawaletsa kuti asatumikire ngati ansembe.*+
64 Amenewa ndi amene mayina awo anawayangʼana mʼkaundula kuti atsimikizire za mzere wawo wobadwira koma sanapezekemo. Choncho anawaletsa kuti asatumikire ngati ansembe.*+