-
Nehemiya 8:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ezara anatsegula bukulo pamaso pa anthu onse, popeza anaima pamalo okwera kusiyana ndi anthu onse. Pamene ankatsegula bukulo, anthu onse anaimirira.
-