Nehemiya 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo anapitiriza kuwerenga bukulo mokweza. Anapitiriza kuwerenga Chilamulo cha Mulungu woona, kuchifotokoza momveka bwino ndi kumveketsa tanthauzo lake. Choncho anathandiza anthuwo kumvetsa tanthauzo la zimene ankawerenga.+ Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:8 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 10 Nsanja ya Olonda,2/1/2006, tsa. 115/15/1996, tsa. 162/15/1986, tsa. 31
8 Iwo anapitiriza kuwerenga bukulo mokweza. Anapitiriza kuwerenga Chilamulo cha Mulungu woona, kuchifotokoza momveka bwino ndi kumveketsa tanthauzo lake. Choncho anathandiza anthuwo kumvetsa tanthauzo la zimene ankawerenga.+
8:8 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 10 Nsanja ya Olonda,2/1/2006, tsa. 115/15/1996, tsa. 162/15/1986, tsa. 31