Nehemiya 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa tsiku lachiwiri, atsogoleri a mabanja a anthu onse, ansembe ndiponso Alevi, anasonkhana pamodzi pamaso pa Ezara wokopera Malemba,* kuti amvetse bwino mawu a mʼChilamulo. Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:13 Nsanja ya Olonda,10/15/1998, tsa. 21
13 Pa tsiku lachiwiri, atsogoleri a mabanja a anthu onse, ansembe ndiponso Alevi, anasonkhana pamodzi pamaso pa Ezara wokopera Malemba,* kuti amvetse bwino mawu a mʼChilamulo.