-
Nehemiya 8:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Analembamonso kuti azilengeza mofuula+ mʼmizinda yonse ndi ku Yerusalemu konse kuti: “Pitani kumapiri mukatenge nthambi za mitengo ya maolivi, nthambi za mitengo ya paini, nthambi za mitengo ya mchisu, mitengo ya kanjedza ndi nthambi za masamba ambiri za mitengo ina kuti mudzamangire misasa mogwirizana ndi zimene zinalembedwa.”
-