Nehemiya 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamene anali ndi njala munawapatsa chakudya chochokera kumwamba+ ndipo pamene anali ndi ludzu munatulutsa madzi pathanthwe.+ Munawauza kuti alowe nʼkutenga dziko limene munalumbira* kuti mudzawapatsa.
15 Pamene anali ndi njala munawapatsa chakudya chochokera kumwamba+ ndipo pamene anali ndi ludzu munatulutsa madzi pathanthwe.+ Munawauza kuti alowe nʼkutenga dziko limene munalumbira* kuti mudzawapatsa.