Nehemiya 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 inu simunawasiye mʼchipululu, chifukwa cha chifundo chanu chachikulu.+ Chipilala cha mtambo sichinawachokere masana ndipo chinkawatsogolera, komanso chipilala cha moto sichinawachokere usiku ndipo chinkawaunikira njira yoyenera kudutsa.+
19 inu simunawasiye mʼchipululu, chifukwa cha chifundo chanu chachikulu.+ Chipilala cha mtambo sichinawachokere masana ndipo chinkawatsogolera, komanso chipilala cha moto sichinawachokere usiku ndipo chinkawaunikira njira yoyenera kudutsa.+