28 Anthu ena onse, ansembe, Alevi, alonda apageti, oimba, atumiki apakachisi ndiponso aliyense amene anadzipatula kwa anthu amʼmayikowo kuti asunge Chilamulo cha Mulungu woona,+ akazi awo, ana awo aamuna ndi aakazi ndiponso aliyense wodziwa zinthu komanso woti akhoza kumvetsa zimene zikunenedwa,