Nehemiya 10:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Komanso kuti sitidzapereka ana athu aakazi kwa anthu amʼdzikoli ndiponso sitidzatenga ana awo aakazi nʼkuwapereka kwa ana athu aamuna.+
30 Komanso kuti sitidzapereka ana athu aakazi kwa anthu amʼdzikoli ndiponso sitidzatenga ana awo aakazi nʼkuwapereka kwa ana athu aamuna.+