Nehemiya 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Seraya mwana wa Hilikiya. Hilikiya anali mwana wa Mesulamu, Mesulamu anali mwana wa Zadoki, Zadoki anali mwana wa Merayoti, Merayoti anali mwana wa Ahitubu,+ mtsogoleri wa panyumba* ya Mulungu woona.
11 Seraya mwana wa Hilikiya. Hilikiya anali mwana wa Mesulamu, Mesulamu anali mwana wa Zadoki, Zadoki anali mwana wa Merayoti, Merayoti anali mwana wa Ahitubu,+ mtsogoleri wa panyumba* ya Mulungu woona.