-
Nehemiya 11:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Abale ake a Adaya, atsogoleri a nyumba za makolo awo, analipo 242. Ndiyeno panalinso Amasisai mwana wa Azareli. Azareli anali mwana wa Azai, Azai anali mwana wa Mesilemoti amene anali mwana wa Imeri.
-