-
Nehemiya 11:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Amasisai pamodzi ndi abale ake, amuna amphamvu ndiponso olimba mtima, analipo okwana 128. Iwowa mtsogoleri wawo anali Zabidiyeli wochokera mʼbanja lotchuka.
-