Nehemiya 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pagulu la Alevi panali awa: Semaya+ mwana wa Hasubu. Hasubu anali mwana wa Azirikamu, Azirikamu anali mwana wa Hasabiya ndipo Hasabiya anali mwana wa Buni.
15 Pagulu la Alevi panali awa: Semaya+ mwana wa Hasubu. Hasubu anali mwana wa Azirikamu, Azirikamu anali mwana wa Hasabiya ndipo Hasabiya anali mwana wa Buni.