Nehemiya 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mfumu inapereka lamulo lokhudza oimba,+ ndipo panali dongosolo loti aziwapatsa thandizo tsiku lililonse mogwirizana ndi zofunikira za tsikulo.
23 Mfumu inapereka lamulo lokhudza oimba,+ ndipo panali dongosolo loti aziwapatsa thandizo tsiku lililonse mogwirizana ndi zofunikira za tsikulo.