Nehemiya 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mʼmasiku a Eliyasibu, Yoyada, Yohanani ndi Yaduwa,+ mayina a atsogoleri a nyumba za makolo za Alevi, ankawalemba ngati mmene ankachitira ndi ansembe mpaka kudzafika mʼnthawi ya ufumu wa Dariyo wa ku Perisiya.
22 Mʼmasiku a Eliyasibu, Yoyada, Yohanani ndi Yaduwa,+ mayina a atsogoleri a nyumba za makolo za Alevi, ankawalemba ngati mmene ankachitira ndi ansembe mpaka kudzafika mʼnthawi ya ufumu wa Dariyo wa ku Perisiya.