-
Nehemiya 12:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Alevi amene anali atsogoleri a nyumba za makolo ankalembedwa mʼbuku la zochitika za pa nthawi imeneyo mpaka kudzafika mʼmasiku a Yohanani, mwana wa Eliyasibu.
-