Nehemiya 12:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anthu amenewa ankatumikira mʼmasiku a Yoyakimu mwana wa Yesuwa+ amene anali mwana wa Yozadaki, komanso mʼmasiku a Nehemiya amene anali bwanamkubwa, ndi Ezara+ amene anali wansembe komanso wokopera Malemba.
26 Anthu amenewa ankatumikira mʼmasiku a Yoyakimu mwana wa Yesuwa+ amene anali mwana wa Yozadaki, komanso mʼmasiku a Nehemiya amene anali bwanamkubwa, ndi Ezara+ amene anali wansembe komanso wokopera Malemba.