Nehemiya 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zitatero ndinalamula kuti ayeretse zipinda zosungira katundu.* Kenako ndinabwezera pamalo pake ziwiya za mʼnyumba ya Mulungu+ woona komanso zopereka zambewu ndi lubani.+
9 Zitatero ndinalamula kuti ayeretse zipinda zosungira katundu.* Kenako ndinabwezera pamalo pake ziwiya za mʼnyumba ya Mulungu+ woona komanso zopereka zambewu ndi lubani.+