Nehemiya 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi izi si zimene makolo anu anachita, moti Mulungu wathu anabweretsa tsoka lonseli pa ife ndi mzindawu? Ndiye inu mukuchititsa kuti akwiyire kwambiri Aisiraeli poipitsa Sabata?”+
18 Kodi izi si zimene makolo anu anachita, moti Mulungu wathu anabweretsa tsoka lonseli pa ife ndi mzindawu? Ndiye inu mukuchititsa kuti akwiyire kwambiri Aisiraeli poipitsa Sabata?”+