Nehemiya 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno ndinawayeretsa ku zinthu zonse zodetsa za anthu a mitundu ina. Komanso ndinapereka ntchito kwa ansembe ndi Alevi, aliyense ndinamʼpatsa ntchito yake.+
30 Ndiyeno ndinawayeretsa ku zinthu zonse zodetsa za anthu a mitundu ina. Komanso ndinapereka ntchito kwa ansembe ndi Alevi, aliyense ndinamʼpatsa ntchito yake.+