Esitere 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mʼchaka chachitatu cha ulamuliro wake, Ahasiwero anakonzera phwando akalonga ndi atumiki ake onse. Asilikali a Perisiya+ ndi Mediya,+ anthu olemekezeka ndiponso akalonga amʼzigawo za ufumu wake analinso pomwepo. Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:3 Nsanja ya Olonda,3/1/2006, tsa. 93/15/1986, tsa. 24
3 Mʼchaka chachitatu cha ulamuliro wake, Ahasiwero anakonzera phwando akalonga ndi atumiki ake onse. Asilikali a Perisiya+ ndi Mediya,+ anthu olemekezeka ndiponso akalonga amʼzigawo za ufumu wake analinso pomwepo.