-
Esitere 1:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndipo kwa masiku ambiri, masiku okwana 180, iye anaonetsa anthuwo chuma chimene chinkachititsa kuti anthu azimulemekeza mu ufumu wake. Anawaonetsanso chuma ndi ulemerero wa ufumu wakewo.
-