Esitere 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nayenso Mfumukazi Vasiti+ anakonzera phwando azimayi kunyumba yachifumu ya Mfumu Ahasiwero.