-
Esitere 1:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Mfumu inawafunsa kuti: “Mogwirizana ndi malamulo, kodi tichite chiyani ndi Mfumukazi Vasiti popeza sanamvere zimene Mfumu Ahasiwero yanena kudzera mwa nduna zake?”
-