Esitere 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Memukani anauza mfumu ndi akalonga kuti: “Mfumukazi Vasiti sanalakwire mfumu yokha,+ koma walakwiranso akalonga onse ndi anthu onse amʼzigawo zonse za Mfumu Ahasiwero.
16 Memukani anauza mfumu ndi akalonga kuti: “Mfumukazi Vasiti sanalakwire mfumu yokha,+ koma walakwiranso akalonga onse ndi anthu onse amʼzigawo zonse za Mfumu Ahasiwero.