-
Esitere 1:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Chifukwa zimene mfumukazi yachita zidziwika kwa akazi onse okwatiwa ndipo ayamba kunyoza amuna awo nʼkumanena kuti, ‘Mfumu Ahasiwero anaitana Mfumukazi Vasiti, koma Vasiti anakana.’
-