-
Esitere 1:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Lero akazi a akalonga a Perisiya ndi Mediya amene amva zimene mfumukazi yachita, alankhula za zimenezi ndi amuna awo ndipo zichititsa kuti ayambe kunyozana kwambiri ndiponso kukwiyitsana.
-