-
Esitere 1:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Anthu akamva za lamulo limene muperekeli mu ufumu wanu wonse, womwe ndi waukulu, akazi onse okwatiwa azilemekeza amuna awo, kaya amunawo ndi olemekezeka kapena anthu wamba.”
-