22 Choncho mfumu inatumiza makalata mʼzigawo zonse za ufumu wake.+ Chigawo chilichonse anachilembera mogwirizana ndi kalembedwe ka anthu akumeneko ndiponso chilankhulo chawo. Anachita izi kuti mwamuna aliyense azitsogolera banja lake ndiponso kuti banjalo lizilankhula chilankhulo cha mwamunayo.