Esitere 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako mkwiyo wa Mfumu Ahasiwero+ utachepa, anakumbukira zimene Vasiti anachita,+ komanso chilango chimene anapatsidwa.+
2 Kenako mkwiyo wa Mfumu Ahasiwero+ utachepa, anakumbukira zimene Vasiti anachita,+ komanso chilango chimene anapatsidwa.+