-
Esitere 2:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Tsiku lililonse Moredikayi ankadutsa kutsogolo kwa bwalo la nyumba ya akazi kuti adziwe ngati Esitere ali bwino komanso zimene zikumuchitikira.
-