-
Esitere 2:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Akatero mtsikana aliyense ankapita kwa mfumu. Akamachoka kunyumba ya akazi kupita kunyumba ya mfumu, ankamupatsa chilichonse chimene wapempha.
-