-
Esitere 2:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Kenako mfumu inakonzera akalonga ake ndi atumiki ake onse phwando lalikulu, phwando la Esitere. Ndiyeno mfumu inamasula akaidi amʼzigawo zake zonse, ndipo inayamba kupereka mphatso mogwirizana ndi chuma chimene mfumuyo inali nacho.
-