Esitere 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ankamufunsa zimenezi tsiku ndi tsiku koma iye sankawamvera. Kenako anthuwo anauza Hamani kuti aone ngati khalidwe la Moredikayi lingalekereredwe+ popeza iye anali atawauza kuti anali Myuda.+ Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:4 Nsanja ya Olonda,3/1/2006, tsa. 10
4 Ankamufunsa zimenezi tsiku ndi tsiku koma iye sankawamvera. Kenako anthuwo anauza Hamani kuti aone ngati khalidwe la Moredikayi lingalekereredwe+ popeza iye anali atawauza kuti anali Myuda.+