Esitere 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ngati mungakonde mfumu, palembedwe lamulo loti anthu amenewa aphedwe. Ine ndidzapereka ndalama zokwana matalente* 10,000 asiliva kwa akuluakulu ogwira ntchito kunyumba ya mfumu kuti akaziike mosungiramo chuma cha mfumu.”* Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:9 Tsanzirani, tsa. 131 Nsanja ya Olonda,10/1/2011, tsa. 21
9 Ngati mungakonde mfumu, palembedwe lamulo loti anthu amenewa aphedwe. Ine ndidzapereka ndalama zokwana matalente* 10,000 asiliva kwa akuluakulu ogwira ntchito kunyumba ya mfumu kuti akaziike mosungiramo chuma cha mfumu.”*