-
Esitere 4:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndiyeno Esitere anaitana Hataki, mmodzi wa amuna ofulidwa a mfumu amene mfumuyo inamuika kuti azitumikira Esitere. Ndipo anamutuma kwa Moredikayi kuti akafufuze zimene zachitika.
-