-
Esitere 5:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndiyeno mfumu inauza atumiki ake kuti: “Pitani mukamuuze Hamani kuti abwere mofulumira mogwirizana ndi zimene Esitere wapempha.” Choncho mfumu ndi Hamani anapita kuphwando limene Esitere anakonza.
-