Esitere 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa nthawi yomwe ankamwa vinyo paphwandolo, mfumu inafunsa Esitere kuti: “Ukufuna kupempha chiyani? Chimene ukufuna ndikupatsa. Ukufuna ndikupatse chiyani? Ngakhale utapempha hafu ya ufumu wangawu, ndikupatsa.”+
6 Pa nthawi yomwe ankamwa vinyo paphwandolo, mfumu inafunsa Esitere kuti: “Ukufuna kupempha chiyani? Chimene ukufuna ndikupatsa. Ukufuna ndikupatse chiyani? Ngakhale utapempha hafu ya ufumu wangawu, ndikupatsa.”+