-
Esitere 6:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndiyeno mfumu inafunsa kuti: “Kodi Moredikayi analandira ulemu wotani chifukwa cha zimene anachitazi?” Atumiki a mfumu anayankha kuti: “Palibe chilichonse chimene anachitiridwa.”
-