Esitere 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atumiki a mfumu anati: “Pabwalo pali Hamani.”+ Ndiyeno mfumu inati: “Muuzeni alowe.”