-
Esitere 6:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndiyeno chovalacho ndi hatchiyo azipereke kwa mmodzi wa akalonga olemekezeka a mfumu. Kenako aveke chovalacho munthu amene mfumu ikufuna kumupatsa ulemuyo ndipo amukweze pahatchiyo nʼkumuyendetsa mʼbwalo la mzinda. Ndiye azifuula patsogolo pake kuti, ‘Izi ndi zimene timachitira munthu amene mfumu yafuna kumʼpatsa ulemu!’”+
-