Esitere 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho Hamani anatenga chovala ndi hatchi, ndipo anaveka Moredikayi+ chovalacho. Kenako anamʼkweza pahatchiyo nʼkumuyendetsa mʼbwalo la mzinda, akufuula patsogolo pake kuti: “Izi ndi zimene timachitira munthu amene mfumu yafuna kumʼpatsa ulemu!”
11 Choncho Hamani anatenga chovala ndi hatchi, ndipo anaveka Moredikayi+ chovalacho. Kenako anamʼkweza pahatchiyo nʼkumuyendetsa mʼbwalo la mzinda, akufuula patsogolo pake kuti: “Izi ndi zimene timachitira munthu amene mfumu yafuna kumʼpatsa ulemu!”