-
Esitere 7:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Zitatero, Mfumu Ahasiwero anafunsa Mfumukazi Esitere kuti: “Wachita zimenezo ndi ndani? Ali kuti munthu amene walimba mtima kuchita zimenezo?”
-