Esitere 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kuwonjezera pamenepo, Esitere analankhulanso ndi mfumu. Iye anagwada pamapazi a mfumuyo ndipo anachonderera kuti mfumu isinthe chiwembu chimene Hamani, mbadwa ya Agagi, anakonzera Ayuda.+ Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:3 Tsanzirani, ptsa. 143-144 Nsanja ya Olonda,1/1/2012, ptsa. 28-29
3 Kuwonjezera pamenepo, Esitere analankhulanso ndi mfumu. Iye anagwada pamapazi a mfumuyo ndipo anachonderera kuti mfumu isinthe chiwembu chimene Hamani, mbadwa ya Agagi, anakonzera Ayuda.+