-
Esitere 8:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako Esitere ananena kuti: “Ngati mungavomereze mfumu, ndipo ngati mungandikomere mtima, komanso ngati inu mfumu mukuona kuti nʼzoyenera ndipo mukusangalala nane, palembedwe lamulo lofafaniza zimene zinalembedwa mʼmakalata amene munthu wachiwembu Hamani,+ mwana wa Hamedata mbadwa ya Agagi,+ analemba pofuna kupha Ayuda amene ali mʼzigawo zanu zonse mfumu.
-