Esitere 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho Mfumu Ahasiwero anauza Mfumukazi Esitere ndi Moredikayi Myuda kuti: “Nyumba ya Hamani ndaipereka kwa Esitere,+ ndipo Hamaniyo ndinalamula kuti apachikidwe pamtengo+ chifukwa anakonza chiwembu choti aphe Ayuda.
7 Choncho Mfumu Ahasiwero anauza Mfumukazi Esitere ndi Moredikayi Myuda kuti: “Nyumba ya Hamani ndaipereka kwa Esitere,+ ndipo Hamaniyo ndinalamula kuti apachikidwe pamtengo+ chifukwa anakonza chiwembu choti aphe Ayuda.