Esitere 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zimene analemba mʼmakalatawo anazipereka kuti zikhale lamulo mʼzigawo zonse. Analengeza kwa anthu a mitundu yonse nʼcholinga choti Ayuda akonzekere kudzabwezera adani awo pa tsiku limeneli.+ Esitere Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:13 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,3/2016, tsa. 3
13 Zimene analemba mʼmakalatawo anazipereka kuti zikhale lamulo mʼzigawo zonse. Analengeza kwa anthu a mitundu yonse nʼcholinga choti Ayuda akonzekere kudzabwezera adani awo pa tsiku limeneli.+