Esitere 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ayuda anasonkhana mʼmizinda yawo mʼzigawo zonse za Mfumu Ahasiwero+ kuti amenyane ndi adani awo amene ankafuna kuwapha. Ndipo palibe munthu amene anakwanitsa kulimbana nawo chifukwa anthu a mitundu yonse ankaopa Ayudawo.+
2 Ayuda anasonkhana mʼmizinda yawo mʼzigawo zonse za Mfumu Ahasiwero+ kuti amenyane ndi adani awo amene ankafuna kuwapha. Ndipo palibe munthu amene anakwanitsa kulimbana nawo chifukwa anthu a mitundu yonse ankaopa Ayudawo.+